It's Driemo (Ndizapereke moyo wanga) Oh, mtima uwupereke Kwa ine ndiwutenge Don't you worry about safety Ndidzachengetera chengetera chengetera I know mtima unaswekapo You've been there unalirapo Ululu mumtima kufikapo Ukaganizira ganizira ganizira Pa iwe ndilola ndipepere Chikondi chisaperewere Olo pa ground paterere I'll love you the same baby Oh udzandifunse Nkadzakuswera mtima udzandifunse Kuti mwina compensation Ndidzapereke moyo wanga Oh, udzandifunse Nkadzakuswera mtima udzandifunse Kuti mwina compensation Ndidzapereke moyo wanga Oh, yeah yeah Don't be scared to love me more Zakale zapita it's me and you Undiuze pomwe pali mantha ako I know mtima umakana ukandiwunika Umaona ngati aja anakunamiza koma I wanna be your soldier Your fighter, protector, defender I just wanna be your friend for life oh Oh, udzandifunse Nkadzakuswera mtima udzandifunse Kuti mwina compensation Ndidzapereke moyo wanga Oh, udzandifunse Nkadzakuswera mtima udzandifunse Kuti mwina compensation Ndidzapereke moyo wanga Oh, yeah yeah Ooh, udzandifunse Udzandifunse Mwina compensation ndidzapereke moyo wanga Oh, udzandifunse Nkadzakuswera mtima udzandifunse Kuti mwina compensation Ndidzapereke moyo wanga Oh, udzandifunse Nkadzakuswera mtima udzandifunse Kuti mwina compensation Ndidzapereke moyo wanga Oh, yeah yeah Oh, udzandifunse Udzandifunse Mwina compensation ndidzapereke moyo wanga Oh, udzandifunse Udzandifunse Mwina compensation ndidzapereke moyo wanga Yeah, heh eeh