Ulemelero wanu Ukale nthawi zonse Ambuye Kondwelani Ndi ntchito ya manja anu Ulemelero wanu Ukale nthawi zonse Ambuye Kondwelani Ndi ntchito ya manja anu Ine ndiza Kuimbirani Ndikadali ndi moyo Ndizalemekeza inu Ndi umunthu wanga onse Ine ndiza Kuimbirani Ndikadali ndi moyo Ndizalemekeza inu Ndi umunthu wanga onse Ulemelero wanu Ukale nthawi zonse Ambuye Kondwelani (oh) Ndi ntchito ya manja anu Ulemelero wanu Ukale nthawi zonse Ambuye Kondwelani Ndi ntchito ya manja anu Oh, ife tiza Kuimbirani Tikadali ndi moyo Tizalemekeza inu Ndi umunthu wathu onse Ife tiza Kuimbirani Tikadali ndi moyo Tizalemekeza inu Ndi umunthu wathu onse Ndipo Mulungu Agade Agade Agade, agade Mulungu agade Salephela Ana Iye Mulungu Agade Agade Agade, agade Mulungu agade Salephela Ana Kodi ndiye Alefa, Omega Oyamba, osiliza Wachipulumutso cha moyo wanga Oh, Iye Mulungu Agade Agade Agade, agade Mulungu agade Salephela Ana Iye ndiye Alefa, Omega Oyamba, osiliza Wachipulumutso cha moyo wanga Oh, Iye Mulungu Agade Agade Agade, agade Mulungu agade Salephela Ana Munalenga munthu M’chifaniziro chanu Ambuye Kondwelani ndi ntchito Ya manja anu Munalenga munthu M’chifaniziro chanu Ambuye Kondwelani ndi ntchito Ya manja anu Ife tiza Kuimbirani Tikadali ndi moyo Tizalemekeza inu Ndi umunthu wathu onse Ife tiza Kuimbirani Tikadali ndi moyo Tizalemekeza inu Ndi umunthu wathu onse