Pobwela pa nyumba panga uyenela ku nkala ndi ulemu Cifukwa ngati ulibe ulemu nizakupanga Ngozi Ine ndikonda antu a ulemu Cifukwa ine niziba kucaya tu mambama twabwino Tiza cita cani Kwa inu anzatu Kuti mupeleke ulemu kwanzanu Tiza cita cani Kwa inu anzatu Kuti mupeleke ulemu kwanzanu Pobwela pa nyumba uyenela ku nkala ndi ulemu Cifukwa bena sibafuna vo kambakamba Vo kambakamba vi leta pamulomo Cifukwa bena baziba kuyasha tukopo twa ngozi Tiza cita cani Kwa inu anzatu Kuti mupeleke ulemu kwanzanu Tiza cita cani Kwa inu anzatu Kuti mupeleke ulemu kwanzanu Tiza cita cani Kwa inu anzatu Kuti mupeleke ulemu kwanzanu Peleka ulemu Bena bacaya Ngozi yovuta Kukopo [?] Tiza cita cani Kwa inu anzatu Kuti mupeleke ulemu kwanzanu Tiza cita cani Kwa inu anzatu Kuti mupeleke ulemu kwanzanu Tiza cita cani Kwa inu anzatu Kuti mupeleke ulemu kwanzanu Pobwela pa nyumba panga uyenela ku nkala ndi ulemu Cifukwa, ine sinifuna vo kambakamba Vo kambakamba vi leta pamulomo Cifukwa bena baziba kuyasha tukopo twa ngozi Tiza cita cani Kwa inu anzatu Kuti mupeleke ulemu kwanzanu Tiza cita cani Kwa inu anzatu Kuti mupeleke ulemu kwanzanu Tiza cita cani Kwa inu anzatu Kuti mupeleke ulemu kwanzanu