Daily Daily daily daily Daily Daily daily daily Theresa Phondo Esther Chungu Tio mwana waku mmawa Odi odi I’m calling Nikuti konkonko Olo kodi when I am falling Yesu enkonto iyo Jehovah (Jehovah) Alinaiwe, mu BM olo Benz Or njinga uma chova (Jehovah) Ali na iwe Ali na ine eh Dai-dai-daily Atuma angelo asamale ine Dai-dai-daily Ndikasochera andilondolera Dai-dai-daily Atuma angelo asamale ine eh, eh Daily daily Sangandisiye ndekha Sangandi ponye ponye paliponse Sangandisiye ndekha Andimenyela nkhondo zakumdima Sangandisiye ndekha Sangandi ponye ponye paliponse Sangandisiye ndekha Andimenyela nkhondo zakumdima Dai-dai-daily Dai-dai-daily Dai-dai-daily Dai-dai-daily Dai-dai-daily Anikonda Yesu yo (yelele yelele) Samagona pali ineh Ani sunga Yesu yo (yelele yelele) Anafa kuti ninkale na umoyo I am blessed and favored oh (Blessed and favored oh) I’m a child of the King Peace and joy on overflow (Joy on overflow) Ndine okondewa Satopa kundiyang’anira Usiku ndi usana kundisamalira My Lord and Savior Yesu yo Yesu yo inu Yesu yo Satopa kundiyang’anira Usiku ndi usana kundisamalira My Lord and Savior Yesu yo Yesu yo Yesu yo oh Dai-dai-daily Atuma angelo asamale ine Dai-dai-daily Ndikasochera andilondolera Dai-dai-daily Atuma angelo asamale ine Daily daily Sangandisiye ndekha Sangandi ponye ponye paliponse Sangandisiye ndekha Andimenyela nkhondo zakumdima Sangandisiye ndekha Sangani ponye ponye paliponse Sangandisiye ndekha Andimenyela nkhondo zakumdima Dai-dai-daily Hey daily daily oh Daily daily oh Dai-dai-daily Daily daily oh Daily daily oh Dai-dai-daily Sangandisiye ndekha Sangandisiye ndekha Daily daily oh Daily daily oh