Sagona tulo Mpulumtsi wa moyo wanga Sagona tulo Ayenda nane sangandisiye ndekha ah Amakhala nane Yehovah anditsogolera Chiuta andilimbikitsa Dai-dai-daily Atuma angelo asamale ine Dai-dai-daily Ndikasochera andilondolera Dai-dai-daily Atuma angelo asamale ine eh, eh Daily daily Sangandisiye ndekha Sangandi ponye ponye paliponse Sangandisiye ndekha Andimenyela nkhondo zakumdima Sangandisiye ndekha Sangandi ponye ponye paliponse Sangandisiye ndekha Andimenyela nkhondo zakumdima Dai-dai-daily Dai-dai-daily Dai-dai-daily Dai-dai-daily Dai-dai-daily Satopa kundiyang’anira Usiku ndi usana kundisamalira My Lord and Savior Yesu yo Yesu yo inu Yesu yo Satopa kundiyang’anira Usiku ndi usana kundisamalira My Lord and Savior Yesu yo Yesu yo Yesu yo oh Dai-dai-daily Atuma angelo asamale ine Dai-dai-daily Ndikasochera andilondolera Dai-dai-daily Atuma angelo asamale ine Daily daily Sangandisiye ndekha Sangandi ponye ponye paliponse Sangandisiye ndekha Andimenyela nkhondo zakumdima Sangandisiye ndekha Sangani ponye ponye paliponse Sangandisiye ndekha Andimenyela nkhondo zakumdima Dai-dai-daily Hey daily daily oh Daily daily oh Dai-dai-daily Daily daily oh Daily daily oh Dai-dai-daily Sangandisiye ndekha Sangandisiye ndekha Daily daily oh Daily daily oh