Wandibalalisa
Zenko B
Mm, yee, no, no, no, koma
Zenko B
Owo, Nelisa
Wandibalalisa
Nzeru zanga wamaliza
Iwe na ine tikwatulane
Owo, Nelisa
Wandibalalisa
Nzeru zanga wamaliza
Iwe na ine tikwatulane, yee, yee
'Ndiwe umandinvetsa kukoma, ine
Ndimaona ndikagona, ndiwe
Ka thupi kako kokoma, hy, ndisaname
Ndimakufila, dona
Akanapanda kukulenga, bwenzi ndili single
Bwenzi ndikuona akazi opanda ntchito, aah
Koma poti ulipo pompano pa dziko, ine
Ndikusakasaka mpaka kumene iwe uliko
Ndimati ndikakuona, chimwemwe udzaza tsaya
Mwayi umenewu ena anautaya
Komano ine ndakupeza, ndikugwilitsitse
Moti ine ndi wako, wina asakupusitsea
(Kolasi)
Owo, Nelisa
Wandibalalisa
Nzeru zanga wamaliza
Iwe na ine tikwatulane
Owo, Nelisa
Wandibalalisa
Nzeru zanga wamaliza
Iwe na ine tikwatulane, yee, yee
Ndikuthokoza Mulungu pondipasa ka ngenge
Moti chaka chino, basi ndikatenge
Ndikaulemu, komanso kopanda phuma
Abale, ndisaname, ine ndapeza ka tsuna
Pa two tayesela kuchotsa one
Undiuze kodi aswer upeza chani?
Kukongola kwako, mndani angachite makani?
Ndimakuuza kuti ndiwe number one
(Kolasi)
Owo, Nelisa
Wandibalalisa
Nzeru zanga wamaliza
Iwe na ine tikwatulane
Owo, Nelisa
Wandibalalisa
Nzeru zanga wamaliza
Iwe na ine tikwatulane, yee, yee
Zenko B
Production Records
Ayi