Sagona tulo
Mpulumtsi wa moyo wanga
Sagona tulo
Ayenda nane sangandisiye ndekha ah
Amakhala nane
Yehovah anditsogolera
Chiuta andilimbikitsa
Dai-dai-daily
Atuma angelo asamale ine
Dai-dai-daily
Ndikasochera andilondolera
Dai-dai-daily
Atuma angelo asamale ine eh, eh
Daily daily
Sangandisiye ndekha
Sangandi ponye ponye paliponse
Sangandisiye ndekha
Andimenyela nkhondo zakumdima
Sangandisiye ndekha
Sangandi ponye ponye paliponse
Sangandisiye ndekha
Andimenyela nkhondo zakumdima
Dai-dai-daily
Dai-dai-daily
Dai-dai-daily
Dai-dai-daily
Dai-dai-daily
Satopa kundiyang’anira
Usiku ndi usana kundisamalira
My Lord and Savior Yesu yo Yesu yo inu Yesu yo
Satopa kundiyang’anira
Usiku ndi usana kundisamalira
My Lord and Savior Yesu yo Yesu yo Yesu yo oh
Dai-dai-daily
Atuma angelo asamale ine
Dai-dai-daily
Ndikasochera andilondolera
Dai-dai-daily
Atuma angelo asamale ine
Daily daily
Sangandisiye ndekha
Sangandi ponye ponye paliponse
Sangandisiye ndekha
Andimenyela nkhondo zakumdima
Sangandisiye ndekha
Sangani ponye ponye paliponse
Sangandisiye ndekha
Andimenyela nkhondo zakumdima
Dai-dai-daily
Hey daily daily oh
Daily daily oh
Dai-dai-daily
Daily daily oh
Daily daily oh
Dai-dai-daily
Sangandisiye ndekha
Sangandisiye ndekha
Daily daily oh
Daily daily oh